Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 3:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Ndidzakupatsani abusa amene amachita zinthu zogwirizana ndi zofuna zanga+ ndipo adzakuthandizani kuti mudziwe zinthu zambiri ndiponso kuti mukhale omvetsa zinthu.

  • Yohane 21:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Atamaliza kudya chakudya chamʼmawacho, Yesu anafunsa Simoni Petulo kuti: “Simoni mwana wa Yohane, kodi umandikonda ine kuposa izi?” Iye anamuyankha kuti: “Inde Ambuye, inunso mukudziwa kuti ndimakukondani kwambiri.” Iye anamuuza kuti: “Dyetsa ana a nkhosa anga.”+

  • Machitidwe 20:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Muzidziyangʼanira nokha+ komanso kusamalira gulu lonse la nkhosa, limene mzimu woyera wakuikani kuti muziliyangʼanira,+ kuti muwete mpingo wa Mulungu,+ umene anaugula ndi magazi a Mwana wake weniweni.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena