Yesaya 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Maonekedwe a nkhope zawo akuwachitira umboni wotsutsana nawo,Ndipo anthuwo akunena za tchimo lawo mofanana ndi anthu a ku Sodomu.+Iwo sanayese nʼkomwe kulibisa. Tsoka kwa iwo, chifukwa akudzibweretsera mavuto.
9 Maonekedwe a nkhope zawo akuwachitira umboni wotsutsana nawo,Ndipo anthuwo akunena za tchimo lawo mofanana ndi anthu a ku Sodomu.+Iwo sanayese nʼkomwe kulibisa. Tsoka kwa iwo, chifukwa akudzibweretsera mavuto.