Yeremiya 30:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Inu mudzakhala anthu anga+ ndipo ine ndidzakhala Mulungu wanu.”+ Yeremiya 32:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Iwo adzakhala anthu anga ndipo ine ndidzakhala Mulungu wawo.+ Zekariya 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndidzawabweretsa, ndipo azidzakhala mu Yerusalemu.+ Iwo adzakhala anthu anga ndipo ine ndidzakhala Mulungu wawo+ woona* ndi wachilungamo.’”
8 Ndidzawabweretsa, ndipo azidzakhala mu Yerusalemu.+ Iwo adzakhala anthu anga ndipo ine ndidzakhala Mulungu wawo+ woona* ndi wachilungamo.’”