Deuteronomo 28:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Mudzalonjeza kukwatira mkazi koma mwamuna wina adzamugwiririra. Mudzamanga nyumba koma simudzakhalamo.+ Mudzadzala mitengo ya mpesa koma simudzadya zipatso zake.+
30 Mudzalonjeza kukwatira mkazi koma mwamuna wina adzamugwiririra. Mudzamanga nyumba koma simudzakhalamo.+ Mudzadzala mitengo ya mpesa koma simudzadya zipatso zake.+