1 Mafumu 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Khonde+ lakutsogolo kwa kachisi* linali mikono 20 mulitali ndipo linkafanana ndi mulifupi mwa nyumbayo. Khondelo linali kutsogolo kwa nyumbayo ndipo linali mikono 10 mulifupi. 2 Mbiri 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Khonde lakutsogolo linali mikono 20 mulitali ndipo linkafanana ndi mulifupi mwa nyumbayo. Kuchoka pansi kufika pamwamba, khondelo linali lalitali mikono 20* ndipo mkati mwake anakutamo ndi golide woyenga bwino.+
3 Khonde+ lakutsogolo kwa kachisi* linali mikono 20 mulitali ndipo linkafanana ndi mulifupi mwa nyumbayo. Khondelo linali kutsogolo kwa nyumbayo ndipo linali mikono 10 mulifupi.
4 Khonde lakutsogolo linali mikono 20 mulitali ndipo linkafanana ndi mulifupi mwa nyumbayo. Kuchoka pansi kufika pamwamba, khondelo linali lalitali mikono 20* ndipo mkati mwake anakutamo ndi golide woyenga bwino.+