2 Mbiri 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kutsata m’litali mwa nyumbayo, kumaso kwake kunali khonde+ la mikono 20 m’litali, mofanana ndi m’lifupi mwa nyumbayo. Kuchoka pansi kufika pamwamba, khondelo linali lalitali mikono 120, ndipo mkati mwake anakutamo ndi golide woyenga bwino.
4 Kutsata m’litali mwa nyumbayo, kumaso kwake kunali khonde+ la mikono 20 m’litali, mofanana ndi m’lifupi mwa nyumbayo. Kuchoka pansi kufika pamwamba, khondelo linali lalitali mikono 120, ndipo mkati mwake anakutamo ndi golide woyenga bwino.