2 Mbiri 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Khonde lakutsogolo linali mikono 20 mulitali ndipo linkafanana ndi mulifupi mwa nyumbayo. Kuchoka pansi kufika pamwamba, khondelo linali lalitali mikono 20* ndipo mkati mwake anakutamo ndi golide woyenga bwino.+
4 Khonde lakutsogolo linali mikono 20 mulitali ndipo linkafanana ndi mulifupi mwa nyumbayo. Kuchoka pansi kufika pamwamba, khondelo linali lalitali mikono 20* ndipo mkati mwake anakutamo ndi golide woyenga bwino.+