1 Mafumu 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Khonde+ la kutsogolo kwa chipinda chachikulu* cha nyumbayo linali mikono 20 m’litali, kufanana ndi m’lifupi mwa nyumbayo. Khondelo linali kutsogolo kwa nyumbayo, ndipo linali mikono 10 m’lifupi mwake. 2 Mbiri 29:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anatseka zitseko+ za khonde, anazimitsa nyale,+ ndiponso anasiya kupsereza zofukiza+ ndi kupereka nsembe zopsereza kwa Mulungu wa Isiraeli m’malo oyera.+
3 Khonde+ la kutsogolo kwa chipinda chachikulu* cha nyumbayo linali mikono 20 m’litali, kufanana ndi m’lifupi mwa nyumbayo. Khondelo linali kutsogolo kwa nyumbayo, ndipo linali mikono 10 m’lifupi mwake.
7 Anatseka zitseko+ za khonde, anazimitsa nyale,+ ndiponso anasiya kupsereza zofukiza+ ndi kupereka nsembe zopsereza kwa Mulungu wa Isiraeli m’malo oyera.+