Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mbiri 28:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Atatero, Davide anapatsa Solomo mwana wake mapulani akamangidwe+ ka khonde+ ndi nyumba zake, zipinda zake zosungiramo katundu,+ zipinda zake zakudenga,*+ zipinda zake zamkati zosalowa kuwala kwambiri, ndi nyumba yokhalamo chivundikiro chophimba machimo.+

  • 2 Mbiri 3:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Kutsata m’litali mwa nyumbayo, kumaso kwake kunali khonde+ la mikono 20 m’litali, mofanana ndi m’lifupi mwa nyumbayo. Kuchoka pansi kufika pamwamba, khondelo linali lalitali mikono 120, ndipo mkati mwake anakutamo ndi golide woyenga bwino.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena