1 Mafumu 6:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Chipinda chamkaticho chinali mikono 20 mulitali, mikono 20 mulifupi ndi mikono 20 kupita mʼmwamba.+ Chipindachi anachikuta ndi golide woyenga bwino, komanso anakuta guwa lansembe+ ndi matabwa a mkungudza. 2 Mbiri 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kenako iye anapanga chipinda cha Malo Oyera Koposa.+ Mulitali mwake chinali mikono 20 mofanana ndi mulifupi mwa nyumbayo ndipo mulifupi mwake chinali mikono 20. Anachikuta ndi golide wabwino wokwana matalente* 600.+
20 Chipinda chamkaticho chinali mikono 20 mulitali, mikono 20 mulifupi ndi mikono 20 kupita mʼmwamba.+ Chipindachi anachikuta ndi golide woyenga bwino, komanso anakuta guwa lansembe+ ndi matabwa a mkungudza.
8 Kenako iye anapanga chipinda cha Malo Oyera Koposa.+ Mulitali mwake chinali mikono 20 mofanana ndi mulifupi mwa nyumbayo ndipo mulifupi mwake chinali mikono 20. Anachikuta ndi golide wabwino wokwana matalente* 600.+