Yeremiya 14:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndiyeno Yehova anandiyankha kuti: “Aneneriwo akulosera zinthu zabodza mʼdzina langa.+ Ine sindinawatume, kuwalamula kapena kulankhula nawo.+ Maulosi amene akukuuzaniwo ndi masomphenya abodza, maulosi opanda pake ndi chinyengo chamumtima mwawo.+ Maliro 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Masomphenya amene aneneri anu anaona ndi abodza komanso achabechabe,+Ndipo sanaulule zolakwa zanu nʼcholinga choti musatengedwe kupita ku ukapolo,+Koma ankaona masomphenya abodza komanso okusocheretsani.+ Ezekieli 13:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Choncho akazi inu simudzaonanso masomphenya abodza ndipo simudzaloseranso zamʼtsogolo.+ Ine ndidzapulumutsa anthu anga mʼmanja mwanu ndipo mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.’”
14 Ndiyeno Yehova anandiyankha kuti: “Aneneriwo akulosera zinthu zabodza mʼdzina langa.+ Ine sindinawatume, kuwalamula kapena kulankhula nawo.+ Maulosi amene akukuuzaniwo ndi masomphenya abodza, maulosi opanda pake ndi chinyengo chamumtima mwawo.+
14 Masomphenya amene aneneri anu anaona ndi abodza komanso achabechabe,+Ndipo sanaulule zolakwa zanu nʼcholinga choti musatengedwe kupita ku ukapolo,+Koma ankaona masomphenya abodza komanso okusocheretsani.+
23 Choncho akazi inu simudzaonanso masomphenya abodza ndipo simudzaloseranso zamʼtsogolo.+ Ine ndidzapulumutsa anthu anga mʼmanja mwanu ndipo mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.’”