Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 26:40
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 40 Kenako adzavomereza zolakwa zawo+ komanso kusakhulupirika ndi zolakwa za makolo awo. Ndipo adzavomereza kuti anachita zinthu mosakhulupirika poyenda motsutsana nane.+

  • Ezekieli 6:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Anthu amene adzapulumuke adzandikumbukira pakati pa anthu amitundu ina amene anawagwira ukapolo.+ Adzazindikira kuti zinandipweteka kwambiri mumtima chifukwa cha mtima wawo wosakhulupirika* womwe unachititsa kuti andipandukire+ komanso maso awo amene amalakalaka mafano awo onyansa.+ Iwo adzachita manyazi komanso kuipidwa chifukwa cha zinthu zonse zoipa ndi zonyansa zimene anachita.+

  • Ezekieli 16:61
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 61 Udzakumbukira khalidwe lako ndipo udzachita manyazi+ ukadzalandira azichemwali ako omwe ndi akulu ako komanso angʼono ako. Ndidzawapereka kwa iwe kuti akhale ana ako aakazi, koma osati chifukwa cha pangano limene ndinachita ndi iwe.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena