Yeremiya 46:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Lengezani zimenezi mu Iguputo, muzilengeze ku Migidoli.+ Lengezani zimenezi ku Nofi* ndi ku Tahapanesi.+ Munene kuti, ‘Imani mʼmalo anu ndipo mukhale okonzeka,Chifukwa lupanga lidzawononga anthu onse amene akuzungulirani. Ezekieli 30:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Lupanga lidzabwera kudzaukira Iguputo, ndipo anthu a ku Itiyopiya adzachita mantha kwambiri anthu akadzaphedwa ku Iguputo.Chuma cha Iguputo chidzalandidwa ndipo maziko ake adzagwetsedwa.+ Ezekieli 32:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndidzachititsa kuti gulu la anthu amene amakutsatira aphedwe ndi malupanga a asilikali amphamvu.Onsewo ndi anthu a mitundu ina omwe ndi ankhanza kwambiri.+ Iwo adzawononga zinthu zimene Iguputo amazinyadira ndipo anthu ambiri amene amamutsatira adzaphedwa.+
14 “Lengezani zimenezi mu Iguputo, muzilengeze ku Migidoli.+ Lengezani zimenezi ku Nofi* ndi ku Tahapanesi.+ Munene kuti, ‘Imani mʼmalo anu ndipo mukhale okonzeka,Chifukwa lupanga lidzawononga anthu onse amene akuzungulirani.
4 Lupanga lidzabwera kudzaukira Iguputo, ndipo anthu a ku Itiyopiya adzachita mantha kwambiri anthu akadzaphedwa ku Iguputo.Chuma cha Iguputo chidzalandidwa ndipo maziko ake adzagwetsedwa.+
12 Ndidzachititsa kuti gulu la anthu amene amakutsatira aphedwe ndi malupanga a asilikali amphamvu.Onsewo ndi anthu a mitundu ina omwe ndi ankhanza kwambiri.+ Iwo adzawononga zinthu zimene Iguputo amazinyadira ndipo anthu ambiri amene amamutsatira adzaphedwa.+