Ezekieli 30:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Lupanga lidzafikadi mu Iguputo,+ ndipo ku Itiyopiya anthu adzamva ululu waukulu. Izi zidzachitika anthu akadzaphedwa mu Iguputo, chuma cha dzikolo chikadzalandidwa komanso maziko ake akadzagwetsedwa.+
4 Lupanga lidzafikadi mu Iguputo,+ ndipo ku Itiyopiya anthu adzamva ululu waukulu. Izi zidzachitika anthu akadzaphedwa mu Iguputo, chuma cha dzikolo chikadzalandidwa komanso maziko ake akadzagwetsedwa.+