Yesaya 19:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 M’tsiku limenelo, Aiguputo adzakhala ngati akazi. Iwo adzanjenjemera+ ndi kuchita mantha, chifukwa Yehova wa makamu adzawatambasulira dzanja lake.+ Ezekieli 32:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndidzachititsa khamu la anthu ako kuphedwa ndi malupanga a anthu amphamvu. Anthu onsewo ndi olamulira ankhanza a mitundu ina ya anthu.+ Iwo adzawononga zonse zimene Iguputo amazinyadira ndipo khamu lake lonse lidzawonongedwa.+
16 M’tsiku limenelo, Aiguputo adzakhala ngati akazi. Iwo adzanjenjemera+ ndi kuchita mantha, chifukwa Yehova wa makamu adzawatambasulira dzanja lake.+
12 Ndidzachititsa khamu la anthu ako kuphedwa ndi malupanga a anthu amphamvu. Anthu onsewo ndi olamulira ankhanza a mitundu ina ya anthu.+ Iwo adzawononga zonse zimene Iguputo amazinyadira ndipo khamu lake lonse lidzawonongedwa.+