Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 55:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Taonani! Ine ndinamuchititsa kuti akhale mboni+ ku mitundu ya anthu,

      Ndiponso kuti akhale mtsogoleri+ ndi wolamulira+ wa mitundu ya anthu.

  • Mateyu 23:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Musamatchulidwenso kuti atsogoleri, chifukwa Mtsogoleri wanu ndi mmodzi, Khristu.

  • Yohane 1:45
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 45 Kenako Filipo anakumana ndi Natanayeli+ nʼkumuuza kuti: “Ife tapeza Yesu, mwana wa Yosefe,+ wa ku Nazareti. Chilamulo cha Mose komanso zimene aneneri analemba zimanena za iyeyu.”

  • Yohane 1:49
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 49 Natanayeli anamuyankha kuti: “Rabi, ndinu Mwana wa Mulungu, ndinu Mfumu ya Isiraeli.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena