Mateyu 27:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tsopano Yesu anaimirira pamaso pa bwanamkubwa ndipo bwanamkubwayo anamufunsa kuti: “Kodi ndiwe Mfumu ya Ayuda?” Yesu anayankha kuti: “Zili choncho, monga mmene mwanenera.”+ Luka 1:31, 32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Tsopano mvetsera! Udzakhala woyembekezera nʼkubereka mwana wamwamuna+ ndipo udzamupatse dzina lakuti Yesu.+ 32 Ameneyu adzakhala wamkulu+ ndipo adzatchedwa Mwana wa Wamʼmwambamwamba.+ Yehova* Mulungu adzamupatsa mpando wachifumu wa Davide atate wake.+ Yohane 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho anatenga nthambi za kanjedza nʼkutuluka kukamuchingamira. Ndipo anayamba kufuula kuti: “Mʼpulumutseni! Wodalitsidwa ndi amene akubwera mʼdzina la Yehova,*+ amene ndi Mfumu ya Isiraeli!”+
11 Tsopano Yesu anaimirira pamaso pa bwanamkubwa ndipo bwanamkubwayo anamufunsa kuti: “Kodi ndiwe Mfumu ya Ayuda?” Yesu anayankha kuti: “Zili choncho, monga mmene mwanenera.”+
31 Tsopano mvetsera! Udzakhala woyembekezera nʼkubereka mwana wamwamuna+ ndipo udzamupatse dzina lakuti Yesu.+ 32 Ameneyu adzakhala wamkulu+ ndipo adzatchedwa Mwana wa Wamʼmwambamwamba.+ Yehova* Mulungu adzamupatsa mpando wachifumu wa Davide atate wake.+
13 Choncho anatenga nthambi za kanjedza nʼkutuluka kukamuchingamira. Ndipo anayamba kufuula kuti: “Mʼpulumutseni! Wodalitsidwa ndi amene akubwera mʼdzina la Yehova,*+ amene ndi Mfumu ya Isiraeli!”+