Mateyu 27:54 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 54 Koma mtsogoleri wa asilikali ndi ena amene anali naye polondera Yesu ataona chivomerezicho ndi zimene zinkachitikazo, anachita mantha kwambiri ndipo anati: “Ndithu, uyu analidi Mwana wa Mulungu.”+ Yohane 1:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Natanayeli anamuyankha kuti: “Rabi, ndinu Mwana wa Mulungu, ndinu Mfumu ya Isiraeli.”+
54 Koma mtsogoleri wa asilikali ndi ena amene anali naye polondera Yesu ataona chivomerezicho ndi zimene zinkachitikazo, anachita mantha kwambiri ndipo anati: “Ndithu, uyu analidi Mwana wa Mulungu.”+