Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 17:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Komabe Ayuda nawonso sanatsatire malamulo a Yehova Mulungu wawo.+ Iwonso ankatsatira miyambo imene Aisiraeli ankatsatira.+

  • Yeremiya 2:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Koma iwe ukunena kuti, ‘Ine ndilibe mlandu uliwonse.

      Ndithudi mkwiyo wake wandichokera.’

      Tsopano ndikukupatsa chiweruzo

      Chifukwa ukunena kuti, ‘Sindinachimwe.’

  • Hoseya 4:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Tamverani mawu a Yehova inu Aisiraeli.

      Yehova ali ndi mlandu ndi anthu amʼdzikoli,+

      Chifukwa mʼdzikoli mulibe choonadi, chikondi chokhulupirika ndipo anthu ake sadziwa Mulungu.+

  • Mika 6:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Inu mapiri akuluakulu, imvani mlandu umene Yehova ali nawo pa anthu ake.

      Mvetserani inu maziko a dziko lapansi,+

      Chifukwa Yehova ali ndi mlandu ndi anthu ake.

      Iye azenga mlandu Aisiraeli, kuti:+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena