Yoweli 2:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Dzuwa lidzasanduka mdima ndipo mwezi udzasanduka magazi,+Tsiku lalikulu ndi lochititsa mantha la Yehova lisanafike.+ Mateyu 24:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Chisautso cha masiku amenewo chikadzangotha, dzuwa lidzachita mdima+ ndipo mwezi sudzapereka kuwala kwake. Nyenyezi zidzagwa kuchokera kumwamba ndipo mphamvu zakumwamba zidzagwedezeka.+ Luka 21:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Komanso padzakhala zizindikiro padzuwa, mwezi ndi nyenyezi.+ Padziko lapansi anthu a mitundu ina adzazunzika chifukwa chothedwa nzeru poona kuti nyanja ikuchita mkokomo komanso kuwinduka. Chivumbulutso 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Nyenyeziyo inatsegula dzenje lolowera kuphompholo ndipo utsi ngati wamungʼanjo yaikulu unatuluka mʼdzenjemo. Dzuwa komanso mpweya zinada+ ndi utsi wamʼdzenjewo.
31 Dzuwa lidzasanduka mdima ndipo mwezi udzasanduka magazi,+Tsiku lalikulu ndi lochititsa mantha la Yehova lisanafike.+
29 Chisautso cha masiku amenewo chikadzangotha, dzuwa lidzachita mdima+ ndipo mwezi sudzapereka kuwala kwake. Nyenyezi zidzagwa kuchokera kumwamba ndipo mphamvu zakumwamba zidzagwedezeka.+
25 Komanso padzakhala zizindikiro padzuwa, mwezi ndi nyenyezi.+ Padziko lapansi anthu a mitundu ina adzazunzika chifukwa chothedwa nzeru poona kuti nyanja ikuchita mkokomo komanso kuwinduka.
2 Nyenyeziyo inatsegula dzenje lolowera kuphompholo ndipo utsi ngati wamungʼanjo yaikulu unatuluka mʼdzenjemo. Dzuwa komanso mpweya zinada+ ndi utsi wamʼdzenjewo.