Zefaniya 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pa tsiku limenelo, sudzachita manyaziChifukwa cha zinthu zonse zimene unachita pondigalukira,+Popeza ndidzachotsa anthu odzikweza pakati panu.Ndipo sudzakhalanso wodzikweza mʼphiri langa lopatulika.+
11 Pa tsiku limenelo, sudzachita manyaziChifukwa cha zinthu zonse zimene unachita pondigalukira,+Popeza ndidzachotsa anthu odzikweza pakati panu.Ndipo sudzakhalanso wodzikweza mʼphiri langa lopatulika.+