Zefaniya 3:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pa tsiku limenelo, sudzachita manyazi chifukwa cha zochita zako zimene unandilakwira nazo,+ pakuti ndidzachotsa pamaso pako anthu odzikweza amene amakhala mosangalala+ ndipo sudzakhalanso wodzikweza m’phiri langa lopatulika.+ Zefaniya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:11 Nsanja ya Olonda,2/15/2001, tsa. 24
11 Pa tsiku limenelo, sudzachita manyazi chifukwa cha zochita zako zimene unandilakwira nazo,+ pakuti ndidzachotsa pamaso pako anthu odzikweza amene amakhala mosangalala+ ndipo sudzakhalanso wodzikweza m’phiri langa lopatulika.+