Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 23:7, 8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Kenako Balamu ananena ndakatulo yakuti:+

      “Balaki mfumu ya Mowabu wandibweretsa kuno kuchokera ku Aramu,+

      Kuchokera kumapiri akumʼmawa kuti:

      ‘Bwera, udzanditembererere Yakobo.

      Bwera, udzaitanire tsoka pa Isiraeli.’+

       8 Ndingathe bwanji kutemberera anthu amene Mulungu sanawatemberere?

      Ndipo ndingathe bwanji kuitanira tsoka anthu amene Yehova sanawaitanire tsoka?+

  • Numeri 24:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Kenako Balaki anapsera mtima Balamu. Ndiyeno Balaki anawomba mʼmanja mokwiya nʼkuuza Balamu kuti: “Ndinakuitana kuti udzatemberere adani anga,+ koma iwe wawadalitsa kwambiri maulendo atatu onsewa.

  • Chivumbulutso 2:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ngakhale zili choncho, ndakupeza ndi milandu ingapo. Iwe kumeneko uli ndi anthu amene akupitiriza kutsatira chiphunzitso cha Balamu,+ amene anaphunzitsa Balaki+ kuti aikire ana a Isiraeli chopunthwitsa kuti adye zoperekedwa nsembe kwa mafano ndi kuchita chiwerewere.*+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena