-
Salimo 44:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Mwachititsa kuti anthu oyandikana nafe azititonza,
Komanso kuti anthu onse amene atizungulira azitinyoza ndi kutiseka.
-
-
Yeremiya 51:51Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
51 “Tachititsidwa manyazi chifukwa tamva mawu onyoza.
-