Salimo 72:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Litamandike dzina lake laulemerero mpaka kalekale,+Ndipo ulemerero wake udzaze dziko lonse lapansi.+ Ame! Ame! Yesaya 11:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Sizidzavulazana+Kapena kuwonongana mʼphiri langa lonse loyera,+Chifukwa dziko lapansi lidzadzaza ndi anthu odziwa YehovaNgati mmene madzi amadzazira mʼnyanja.+ Zekariya 14:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yehova adzakhala Mfumu ya dziko lonse lapansi.+ Pa tsiku limenelo, Yehova adzakhala mmodzi+ ndipo dzina lake lidzakhala limodzi.+
19 Litamandike dzina lake laulemerero mpaka kalekale,+Ndipo ulemerero wake udzaze dziko lonse lapansi.+ Ame! Ame!
9 Sizidzavulazana+Kapena kuwonongana mʼphiri langa lonse loyera,+Chifukwa dziko lapansi lidzadzaza ndi anthu odziwa YehovaNgati mmene madzi amadzazira mʼnyanja.+
9 Yehova adzakhala Mfumu ya dziko lonse lapansi.+ Pa tsiku limenelo, Yehova adzakhala mmodzi+ ndipo dzina lake lidzakhala limodzi.+