-
Salimo 76:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Munapereka chiweruzo muli kumwamba.+
Dziko lapansi linachita mantha ndipo linakhala chete+
-
Salimo 115:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Mulungu wathu ali kumwamba.
Iye amachita chilichonse chimene chamusangalatsa.
-
-
Zekariya 2:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Anthu nonsenu, khalani chete pamaso pa Yehova, chifukwa iye wanyamuka pamalo ake oyera okhala ndipo akufuna kuchitapo kanthu.
-
-
-