Yesaya 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Fuulani mwachisangalalo inu okhala mu Ziyoni,*Chifukwa Woyera wa Isiraeli amene ali pakati panu ndi wamkulu.” Yoweli 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndipo mudzadziwa kuti ine ndine Yehova Mulungu wanu, amene ndimakhala mu Ziyoni, phiri langa lopatulika.+ Yerusalemu adzakhala malo opatulika,+Ndipo anthu achilendo* sadzadutsanso mmenemo.+ Zekariya 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Pa tsiku limenelo mitundu yambiri ya anthu idzakhala kumbali ya Yehova+ ndipo adzakhala anthu anga. Ine ndidzakhala pakati pako.” Ndipo udzadziwa kuti Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wandituma kwa iwe. Zekariya 8:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndidzawabweretsa, ndipo azidzakhala mu Yerusalemu.+ Iwo adzakhala anthu anga ndipo ine ndidzakhala Mulungu wawo+ woona* ndi wachilungamo.’”
6 Fuulani mwachisangalalo inu okhala mu Ziyoni,*Chifukwa Woyera wa Isiraeli amene ali pakati panu ndi wamkulu.”
17 Ndipo mudzadziwa kuti ine ndine Yehova Mulungu wanu, amene ndimakhala mu Ziyoni, phiri langa lopatulika.+ Yerusalemu adzakhala malo opatulika,+Ndipo anthu achilendo* sadzadutsanso mmenemo.+
11 “Pa tsiku limenelo mitundu yambiri ya anthu idzakhala kumbali ya Yehova+ ndipo adzakhala anthu anga. Ine ndidzakhala pakati pako.” Ndipo udzadziwa kuti Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wandituma kwa iwe.
8 Ndidzawabweretsa, ndipo azidzakhala mu Yerusalemu.+ Iwo adzakhala anthu anga ndipo ine ndidzakhala Mulungu wawo+ woona* ndi wachilungamo.’”