Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 1:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Ndidzakupatsaninso oweruza

      Komanso alangizi ngati mmene zinaliri poyamba.+

      Pambuyo pa zimenezi mudzatchedwa Mzinda Wachilungamo komanso Mzinda Wokhulupirika.+

  • Yesaya 60:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ana a anthu amene ankakupondereza adzabwera nʼkudzagwada pamaso pako.

      Anthu onse amene ankakuchitira zachipongwe adzagwada pamapazi ako,

      Ndipo adzakutchula kuti mzinda wa Yehova,

      Ziyoni wa Woyera wa Isiraeli.+

  • Yeremiya 33:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Mʼmasiku amenewo Yuda adzapulumutsidwa+ ndipo Yerusalemu adzakhala mwamtendere.+ Yerusalemu azidzatchulidwa kuti, Yehova Ndi Chilungamo Chathu.’”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena