Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 66:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Mudzaona zimenezi ndipo mtima wanu udzasangalala.

      Mafupa anu adzakhala ndi mphamvu ngati udzu wobiriwira.

      Ndipo dzanja la* Yehova lidzadziwika kwa atumiki ake,

      Koma iye adzakwiyira adani ake.”+

  • Zefaniya 3:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Fuula mosangalala, iwe mwana wamkazi wa Ziyoni!*

      Fuula chifukwa chopambana, iwe Isiraeli!+

      Sangalala ndiponso kondwera ndi mtima wonse, iwe mwana wamkazi wa Yerusalemu!*+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena