Malaki 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Kodi tonsefe atate wathu si mmodzi?+ Kodi si Mulungu mmodzi amene anatilenga? Ndiye nʼchifukwa chiyani tikuchitirana zachinyengo+ nʼkumaipitsa pangano la makolo athu akale?
10 “Kodi tonsefe atate wathu si mmodzi?+ Kodi si Mulungu mmodzi amene anatilenga? Ndiye nʼchifukwa chiyani tikuchitirana zachinyengo+ nʼkumaipitsa pangano la makolo athu akale?