Mateyu 18:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako anawauza kuti: “Ndithu ndikukuuzani, mukapanda kutembenuka*+ nʼkukhala ngati ana aangʼono, simudzalowa mu Ufumu wakumwamba.+ Yohane 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yesu anayankha kuti: “Ndithudi ndikukuuza, munthu sangathe kulowa mu Ufumu wa Mulungu ngati atapanda kubadwa mwa madzi+ ndi mzimu.+
3 Kenako anawauza kuti: “Ndithu ndikukuuzani, mukapanda kutembenuka*+ nʼkukhala ngati ana aangʼono, simudzalowa mu Ufumu wakumwamba.+
5 Yesu anayankha kuti: “Ndithudi ndikukuuza, munthu sangathe kulowa mu Ufumu wa Mulungu ngati atapanda kubadwa mwa madzi+ ndi mzimu.+