Genesis 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Aliyense wopha munthu, nayenso adzaphedwa ndi munthu,*+ chifukwa Mulungu anapanga munthu mʼchifaniziro chake.+ Ekisodo 20:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Musaphe munthu.*+ Deuteronomo 5:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Musaphe munthu.*+
6 Aliyense wopha munthu, nayenso adzaphedwa ndi munthu,*+ chifukwa Mulungu anapanga munthu mʼchifaniziro chake.+