-
Numeri 35:20, 21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Ngati munthu wafa wina atamukankha chifukwa chodana naye, kapena ngati wafa wina atamugenda ndi chinachake ndi zolinga zoipa,*+ 21 kapenanso wafa wina atamumenya ndi dzanja lake chifukwa chodana naye, amene wapha mnzakeyo aphedwe ndithu. Iye ndi wopha munthu. Wobwezera magazi aphe wopha munthuyo akangomupeza.
-