Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 19:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Ine ndikukuuzani kuti aliyense amene wasiya mkazi wake nʼkukwatira wina wachita chigololo, kupatulapo ngati wamusiya chifukwa cha chiwerewere.”*+

  • Maliko 10:11, 12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Iye anawauza kuti: “Aliyense amene wasiya mkazi wake nʼkukwatira wina, wachita chigololo+ ndipo walakwira mkaziyo. 12 Ndipo ngati mkazi wasiya mwamuna wake nʼkukwatiwa ndi wina, wachita chigololo.”+

  • Luka 16:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Aliyense amene wasiya mkazi wake nʼkukwatira wina, wachita chigololo ndipo aliyense amene wakwatira mkazi wosiyidwayo nayenso wachita chigololo.+

  • Aroma 7:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ngati mkaziyo angakwatiwe ndi mwamuna wina mwamuna wake ali moyo, ndiye kuti wachita chigololo.+ Koma ngati mwamuna wake wamwalira, mkaziyo wamasuka ku lamulo lokhudza mwamuna wake, choncho sanachite chigololo ngati atakwatiwa ndi mwamuna wina.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena