Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Luka 6:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 Komanso, siyani kuweruza ena, mukatero inunso simudzaweruzidwa.+ Siyani kutsutsa ena ndipo inunso simudzatsutsidwa. Pitirizani kukhululukira anthu machimo awo ndipo machimo anunso adzakhululukidwa.+

  • Aroma 2:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Choncho kaya ndiwe ndani,+ ngati umaweruza ena, ulibe chifukwa chomveka chodzilungamitsira. Popeza ukamaweruza ena, umakhala ukudzitsutsa wekha, chifukwa iwenso umachita zomwezo.+

  • Aroma 14:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ndiye tisamaweruzane,+ koma mʼmalomwake tsimikizani mtima kuti simukuchita chilichonse chimene chingakhumudwitse kapena kupunthwitsa mʼbale wanu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena