Mateyu 26:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Mawu adakali mʼkamwa, Yudasi, mmodzi wa ophunzira 12 aja, anafika limodzi ndi gulu lalikulu la anthu kuchokera kwa ansembe aakulu ndi kwa akulu, atanyamula malupanga ndi zibonga.+ Yohane 13:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Sindikunena nonsenu, ndikudziwa amene ndawasankha. Koma zimenezi zachitika kuti lemba likwaniritsidwe,+ limene limati: ‘Munthu amene ankadya chakudya changa, watukula chidendene chake nʼkundiukira.’*+
47 Mawu adakali mʼkamwa, Yudasi, mmodzi wa ophunzira 12 aja, anafika limodzi ndi gulu lalikulu la anthu kuchokera kwa ansembe aakulu ndi kwa akulu, atanyamula malupanga ndi zibonga.+
18 Sindikunena nonsenu, ndikudziwa amene ndawasankha. Koma zimenezi zachitika kuti lemba likwaniritsidwe,+ limene limati: ‘Munthu amene ankadya chakudya changa, watukula chidendene chake nʼkundiukira.’*+