Yohane 13:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Sindikunena nonsenu, ndikudziwa amene ndawasankha.+ Koma zili choncho kuti Malemba akwaniritsidwe,+ paja amati, ‘Munthu amene anali kudya chakudya changa wanyamula chidendene chake kundiukira.’+ Yohane Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:18 Yesu—Ndi Njira, tsa. 270 Nsanja ya Olonda,8/15/2011, tsa. 137/1/1990, tsa. 8
18 Sindikunena nonsenu, ndikudziwa amene ndawasankha.+ Koma zili choncho kuti Malemba akwaniritsidwe,+ paja amati, ‘Munthu amene anali kudya chakudya changa wanyamula chidendene chake kundiukira.’+