Mateyu 4:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kuyambira nthawi imeneyo, Yesu anayamba kulalikira kuti: “Lapani, chifukwa Ufumu wakumwamba wayandikira.”+ Luka 10:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 muzichiritsanso odwala amene ali mmenemo komanso muziwauza kuti: ‘Ufumu wa Mulungu wakuyandikirani.’+
17 Kuyambira nthawi imeneyo, Yesu anayamba kulalikira kuti: “Lapani, chifukwa Ufumu wakumwamba wayandikira.”+
9 muzichiritsanso odwala amene ali mmenemo komanso muziwauza kuti: ‘Ufumu wa Mulungu wakuyandikirani.’+