Mateyu 10:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mukapita muzikalalikira kuti, ‘Ufumu wakumwamba wayandikira.’+ Maliko 1:14, 15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Yohane atamangidwa, Yesu anapita ku Galileya+ kukalalikira uthenga wabwino wa Mulungu.+ 15 Iye ankanena kuti: “Nthawi yoikidwiratu yakwana ndipo Ufumu wa Mulungu wayandikira. Lapani+ ndipo mukhulupirire uthenga wabwino!”
14 Yohane atamangidwa, Yesu anapita ku Galileya+ kukalalikira uthenga wabwino wa Mulungu.+ 15 Iye ankanena kuti: “Nthawi yoikidwiratu yakwana ndipo Ufumu wa Mulungu wayandikira. Lapani+ ndipo mukhulupirire uthenga wabwino!”