Luka 6:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Munthu wabwino amatulutsa zabwino mʼchuma chabwino chamumtima mwake, koma munthu woipa amatulutsa zoipa mʼchuma choipa chamumtima mwake, chifukwa pakamwa pamalankhula zosefukira mumtima.+ Yakobo 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Lilimenso ndi moto.+ Pa ziwalo zonse za thupi lathu, lilime ndi lodzaza ndi zinthu zosalungama chifukwa limadetsa thupi lonse+ komanso limayatsa moyo wonse wa munthu* ndipo lili ndi moto wa Gehena.*
45 Munthu wabwino amatulutsa zabwino mʼchuma chabwino chamumtima mwake, koma munthu woipa amatulutsa zoipa mʼchuma choipa chamumtima mwake, chifukwa pakamwa pamalankhula zosefukira mumtima.+
6 Lilimenso ndi moto.+ Pa ziwalo zonse za thupi lathu, lilime ndi lodzaza ndi zinthu zosalungama chifukwa limadetsa thupi lonse+ komanso limayatsa moyo wonse wa munthu* ndipo lili ndi moto wa Gehena.*