Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 12:46
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 46 Ali mkati molankhula ndi gulu la anthulo, kunabwera mayi ake ndi azichimwene ake.+ Iwo anaima panja ndipo ankafuna kuti alankhule naye.+

  • Yohane 2:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Zimenezi zitachitika, Yesu, mayi ake, azichimwene ake+ ndi ophunzira ake anapita ku Kaperenao,+ koma sanakhaleko masiku ambiri.

  • Machitidwe 1:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Mogwirizana, onsewa ankalimbikira kupemphera pamodzi ndi Mariya mayi a Yesu, azimayi ena+ komanso azichimwene ake a Yesu.+

  • 1 Akorinto 9:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Kodi tilibe ufulu woyenda limodzi ndi akazi athu okhulupirira+ ngati mmene amachitira atumwi ena onse, abale awo a Ambuye+ komanso Kefa?*+

  • Agalatiya 1:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Koma atumwi ena onse sindinawaone kupatulapo Yakobo,+ mchimwene wa Ambuye.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena