Mateyu 13:55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 Kodi uyu si mwana wa kalipentala uja?+ Kodi mayi ake si Mariya, ndipo azichimwene ake si Yakobo, Yosefe, Simoni ndi Yudasi?+ Agalatiya 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma atumwi ena onse sindinawaone kupatulapo Yakobo,+ mchimwene wa Ambuye.
55 Kodi uyu si mwana wa kalipentala uja?+ Kodi mayi ake si Mariya, ndipo azichimwene ake si Yakobo, Yosefe, Simoni ndi Yudasi?+