2 Akorinto 1:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Sikuti ndife olamulira chikhulupiriro chanu,+ koma ndife antchito anzanu kuti muzisangalala, popeza ndinu okhazikika chifukwa cha chikhulupiriro chanu. 1 Petulo 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Musamachite zinthu ngati mafumu pakati pa anthu a Mulungu,*+ koma muzipereka chitsanzo chabwino kwa gulu la nkhosa.+
24 Sikuti ndife olamulira chikhulupiriro chanu,+ koma ndife antchito anzanu kuti muzisangalala, popeza ndinu okhazikika chifukwa cha chikhulupiriro chanu.
3 Musamachite zinthu ngati mafumu pakati pa anthu a Mulungu,*+ koma muzipereka chitsanzo chabwino kwa gulu la nkhosa.+