Luka 14:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Yesu anamuuza kuti: “Munthu wina anakonza phwando lalikulu la chakudya chamadzulo+ ndipo anaitana anthu ambiri. Chivumbulutso 19:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mngeloyo anandiuza kuti, “Lemba kuti: Osangalala ndi amene aitanidwa kuchakudya chamadzulo cha phwando la ukwati wa Mwanawankhosa.”+ Anandiuzanso kuti: “Amenewa ndi mawu oona a Mulungu.”
16 Yesu anamuuza kuti: “Munthu wina anakonza phwando lalikulu la chakudya chamadzulo+ ndipo anaitana anthu ambiri.
9 Mngeloyo anandiuza kuti, “Lemba kuti: Osangalala ndi amene aitanidwa kuchakudya chamadzulo cha phwando la ukwati wa Mwanawankhosa.”+ Anandiuzanso kuti: “Amenewa ndi mawu oona a Mulungu.”