Mateyu 22:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Ufumu wakumwamba tingauyerekezere ndi mfumu imene inakonzera mwana wake wamwamuna phwando la ukwati.+ Mateyu 25:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Atanyamuka kupita kukagula mafutawo, mkwati anafika. Anamwali amene anali atakonzeka aja analowa naye limodzi mʼnyumba imene munali phwando laukwati+ ndipo chitseko chinatsekedwa.
2 “Ufumu wakumwamba tingauyerekezere ndi mfumu imene inakonzera mwana wake wamwamuna phwando la ukwati.+
10 Atanyamuka kupita kukagula mafutawo, mkwati anafika. Anamwali amene anali atakonzeka aja analowa naye limodzi mʼnyumba imene munali phwando laukwati+ ndipo chitseko chinatsekedwa.