Mateyu 10:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Musachite mantha ndi amene amapha thupi koma sangathe kupha moyo.+ Mʼmalomwake, muziopa amene angathe kuwononga zonse ziwiri, moyo ndi thupi lomwe mʼGehena.*+ Luka 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Koma ndikuuzani woti muzimuopa: Muziopa Iye amene amati akapha, amakhalanso ndi mphamvu zoponya munthu mʼGehena.*+ Ndithu ndikukuuzani, muziopa Ameneyu.+
28 Musachite mantha ndi amene amapha thupi koma sangathe kupha moyo.+ Mʼmalomwake, muziopa amene angathe kuwononga zonse ziwiri, moyo ndi thupi lomwe mʼGehena.*+
5 Koma ndikuuzani woti muzimuopa: Muziopa Iye amene amati akapha, amakhalanso ndi mphamvu zoponya munthu mʼGehena.*+ Ndithu ndikukuuzani, muziopa Ameneyu.+