Maliko 13:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Khalani maso, khalani tcheru,+ chifukwa simukudziwa kuti nthawi yoikidwiratu idzafika liti.+ 1 Petulo 5:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Khalanibe oganiza bwino ndipo khalani tcheru+ chifukwa mdani wanu Mdyerekezi akuyendayenda ngati mkango wobangula, kuti ameze winawake.*+ Chivumbulutso 16:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Taona! Ndikubwera ngati wakuba.+ Wosangalala ndi amene akukhalabe maso+ ndiponso amene wavalabe malaya ake akunja, kuti asayende wosavala anthu nʼkuona maliseche ake.”+
8 Khalanibe oganiza bwino ndipo khalani tcheru+ chifukwa mdani wanu Mdyerekezi akuyendayenda ngati mkango wobangula, kuti ameze winawake.*+
15 “Taona! Ndikubwera ngati wakuba.+ Wosangalala ndi amene akukhalabe maso+ ndiponso amene wavalabe malaya ake akunja, kuti asayende wosavala anthu nʼkuona maliseche ake.”+