Chivumbulutso 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Choncho ndikukulangiza kuti ugule kwa ine golide woyengedwa ndi moto, kuti ukhale wolemera. Ugulenso zovala zoyera kuti uvale, nʼcholinga choti maliseche ako asaonekere nʼkuchita manyazi.+ Ndiponso ugule mankhwala opaka mʼmaso ako+ kuti uone.+
18 Choncho ndikukulangiza kuti ugule kwa ine golide woyengedwa ndi moto, kuti ukhale wolemera. Ugulenso zovala zoyera kuti uvale, nʼcholinga choti maliseche ako asaonekere nʼkuchita manyazi.+ Ndiponso ugule mankhwala opaka mʼmaso ako+ kuti uone.+