Maliko 14:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Khalani maso ndipo mupitirize kupemphera kuti musalowe mʼmayesero.+ Zoona, mzimu ndi wofunitsitsa, koma thupi ndi lofooka.”+ Aroma 7:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 koma ndimaona lamulo lina mʼthupi* langa likumenyana ndi malamulo amʼmaganizo mwanga+ nʼkundichititsa kukhala kapolo wa lamulo la uchimo+ limene lili mʼthupi* langa.
38 Khalani maso ndipo mupitirize kupemphera kuti musalowe mʼmayesero.+ Zoona, mzimu ndi wofunitsitsa, koma thupi ndi lofooka.”+
23 koma ndimaona lamulo lina mʼthupi* langa likumenyana ndi malamulo amʼmaganizo mwanga+ nʼkundichititsa kukhala kapolo wa lamulo la uchimo+ limene lili mʼthupi* langa.