Zekariya 13:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Iwe lupanga, nyamuka ubaye mʼbusa wanga.+Ubaye munthu yemwe ndi mnzanga,” watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba. “Ipha mʼbusa+ ndipo nkhosa zake zibalalike.+Ine ndidzalanga nkhosa zonyozeka.” Maliko 14:50 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 50 Zitatero ophunzira ake onse anamuthawa nʼkumusiya yekha.+ Yohane 16:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ndithu ndikukuuzani, nthawi ikubwera ndipo yafika kale, pamene nonse mubalalika, aliyense kupita kunyumba kwake ndipo mundisiya ndekha.+ Koma sindikhala ndekha, chifukwa Atate ali ndi ine.+
7 “Iwe lupanga, nyamuka ubaye mʼbusa wanga.+Ubaye munthu yemwe ndi mnzanga,” watero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba. “Ipha mʼbusa+ ndipo nkhosa zake zibalalike.+Ine ndidzalanga nkhosa zonyozeka.”
32 Ndithu ndikukuuzani, nthawi ikubwera ndipo yafika kale, pamene nonse mubalalika, aliyense kupita kunyumba kwake ndipo mundisiya ndekha.+ Koma sindikhala ndekha, chifukwa Atate ali ndi ine.+